TY - BOOK TI - MTANTHAUZIRAMAWU wa Chinyanja /Chichewa SN - 9990817812 PY - 2000/// CY - Blantyre PB - Dzuka Publishing Company KW - Ndi buku loyamba lotanthauzira mawu a mchinyanja mchiyankhulo chomwecho KW - Muli zitsanzo zothyakuka bwino zosonyeza kagwiritsidwe ntchito koyenera ka mawu KW - Masonyezedwe katchulidwe koyenera ka mawu osiyanasiyana N2 - Buku lofunika kwambiri chifukwa pa chitukuko cha chinyanja mdziko lino ndi buku loyamba M'malawi lotanthauzira mawu a Chinyanja mu chiyankhulo chomwecho; Mntanthauziyu ali ndi zinthu zambiri zokhudza Chinyanja zoti ndizofunika kwambiri kwa munthu amene afuna kudziwa kapena kuphunzira za chiyankhulochi ER -