MTANTHAUZIRAMAWU wa Chinyanja /Chichewa
- Blantyre Dzuka Publishing Company 2000
- x, 366p.
Buku lofunika kwambiri chifukwa pa chitukuko cha chinyanja mdziko lino ndi buku loyamba M'malawi lotanthauzira mawu a Chinyanja mu chiyankhulo chomwecho Mntanthauziyu ali ndi zinthu zambiri zokhudza Chinyanja zoti ndizofunika kwambiri kwa munthu amene afuna kudziwa kapena kuphunzira za chiyankhulochi
9990817812
Muli zitsanzo zothyakuka bwino zosonyeza kagwiritsidwe ntchito koyenera ka mawu Masonyezedwe katchulidwe koyenera ka mawu osiyanasiyana